
Lolemba sabata ino, ‘Mbuyache Makawa’ monga momwe amadzitchulira munyimbo zake, watulutsa nyimbo ya tsopano yomwe akuitchula kuti ‘Bosh’ yomwe wajambula ndi Drue G pomwe kanema yake yajambulidwa ndi Mega.
Mu nyimbo ya ‘Bosh’ yomwe tanthauzo lake ndi ‘Bodza’, Makawa akudzudzu makhalidwe omwe a sing’anga akuchita pomabera anthu ndalama pomawanamiza kuti ali ndi mtera osiyanasiyana.
Mu vesi…