Pomwe namatetule wa chamba cha Amapiano, Zeze Kingston walengeza kuti zolandira ma “award” wasiyira ena, anthu ena ati uku nkuwopa kusambitsidwa chokweza ndi woyimba nzake Fada Moti yemwe wayaka moto.
Lachinayi, Zeze watulutsa kalata yofotokoza kuti sakufunaso kumasankhidwa m’mipikisano ya oyimba ofuna kulandira ma award ponena kuti walandira…